BOLESAMA EXAMINATIONS BOARD
2024 END OF TERM 2 EXAMINATION FOR STANDARD 4
SOCIAL STUDIES
(50 Marks)
DATE: Friday. 15 March,2024
DZINA: ______________________________________________________
LANGIZO
Yankhani mafunso onse
GAWO A (20 Malikisi)
1. Tchulani atsogoleri anu a dera la A. Zimathandiza boma kugawa
mfumu ya mpando. chitukuko moyenera.
A. Pulezidenti C. phungu B. Boma limagawa zakudya
B. Nyakwawa D. nduna ya dziko moyenera
2. Ntchito ya mfumu ya mpando ndi C. Anthu amalandira nsapaato
______________ D. Anthu amakolola chakudya
A. Kulamula dziko chambiri
B. Kutsogolera asilikali
C. Kulimbikitsa kuba 6. Ntchito ziwiri zopezera ndalama
D. Kuweruza milandu m’dera lathu ndi ______
A. Kugwira ganyu ndi kuba
3. Ndi zinthu ziwiri ziti zomwe B. Kumenya anthu ndi kugwira ganyu
timagwiritsa ntchito posamalira malo C. Kuchita malonda ndi kuba
amene timatungapo madzi? D. Kugwira ganyu ndi kuchita
A. Masamba ndi masache malonda
B. Madzi ndi masamba
C. Mitengo ndi masache 7. Kodi ndi tizilombo tanji tomwe
D. Masache ndi chikolopa timapezeka nthawi ya dzinja?
A. Ngumbi C. mphemvu
4. Kodi madzi angaonongeke bwanji? B. Nsomba D. sikidzi
A. Pakumwa C. powasefa
B. Pa kukolopa D. kukodzera 8. Zinthu zomwe zimasungidwa mfiliji
mumtsinje ndi monga _________
A. Chimanga ndi makope
5. N,chifukwa chiyani kuli koyenera B. Nsewula ndi khobwe
kudziwa chiwerengero cha anthu C. Nyama ndi mkaka
mdera? D. Ufa ndi mpunga
9. Kodi zikwangwani ndi zofunika 10. Kodi ndi zinthu ziti zomwe
bwanji? zingapezeke mu mtsinje?
A. Zimathandiza kuti ztidzikhonza A. Nsomba
B. Zimakongoletsa malo B. Nthaka ya bwino
C. Zimathandiza ophunzira kukonda C. Udzu
sukulu D. mitengo
D. Zimachepetsa ngozi pa msewu
GAWO B (30 Malikisi)
11. a. kodi zikwangwani tingazisamalire bwanji?
________________________________________________________________________
___________________________________________________________________ 2mks
b. Tchulani mitundu iwiri ya zikwangwani za pa msewu.
________________________________________________________________________
___________________________________________________________________4mks)
12. a. Tchulani zolimidwa ziwiri zomwe zimalimidwa mdera lanu.
________________________________________________________________________
___________________________________________________________________4mks)
b. Fotokozani njira ziwiri za makolo zotetezera zakudya kuti zisaonongeke.
________________________________________________________________________
___________________________________________________________________4mks)
13. Perekani zifukwa ziwiri zimene mmadera ena muli anthu ochuluka.
________________________________________________________________________
___________________________________________________________________4mks)
14. [Link] mitundu iwiri ya anthu opezeka mdera lanu
________________________________________________________________________
___________________________________________________________________4mks)
[Link] ntchito ziwiri za madzi.
________________________________________________________________________
___________________________________________________________________4mks)
15. Tchulani njira ziwiri za makono zosungira zakudya.
________________________________________________________________________
___________________________________________________________________4mks)
MAFUNSO ATHERA PANO
BOLERASAMA PRODUCTION