0% found this document useful (0 votes)
241 views2 pages

Malawi MOH HPV Leaflet Chichewa 2013

The document discusses HPV vaccination and cervical cancer prevention in Malawi. It states that three girls received HPV vaccines, with the first receiving it, the second after two months, and the third after four months after the second. It encourages teachers to inform female students about HPV vaccination to prevent cervical cancer, and encourages chiefs and mothers to support girls getting vaccinated. HPV is transmitted through sexual contact and can cause cervical cancer if untreated. The vaccine protects against HPV infection and is provided to all girls in standard 4 in schools, and to girls over 10 at hospitals and health centers.

Uploaded by

Jefferson_mario
Copyright
© © All Rights Reserved
We take content rights seriously. If you suspect this is your content, claim it here.
Available Formats
Download as PDF, TXT or read online on Scribd
0% found this document useful (0 votes)
241 views2 pages

Malawi MOH HPV Leaflet Chichewa 2013

The document discusses HPV vaccination and cervical cancer prevention in Malawi. It states that three girls received HPV vaccines, with the first receiving it, the second after two months, and the third after four months after the second. It encourages teachers to inform female students about HPV vaccination to prevent cervical cancer, and encourages chiefs and mothers to support girls getting vaccinated. HPV is transmitted through sexual contact and can cause cervical cancer if untreated. The vaccine protects against HPV infection and is provided to all girls in standard 4 in schools, and to girls over 10 at hospitals and health centers.

Uploaded by

Jefferson_mario
Copyright
© © All Rights Reserved
We take content rights seriously. If you suspect this is your content, claim it here.
Available Formats
Download as PDF, TXT or read online on Scribd
You are on page 1/ 2

katemera

wa khansa
ya khomo
Mtsikana amalandira katemerayu katatu.
la chibelekero
Akalandira oyamba,
?
wachiwiri amalandira pakatha miyezi iwiri.
?
Omaliza amalandira pakatha miyezi inayi atalandira
?
wachiwiri
Uthenga wapadera:
? Aphunzitsi, onetsetsani kuti atsikana onse a
standade 4 alandira katemera wa HPV kuti
atetezedwe ku khansa ya khomo lachiberekero
? Aphunzitsi fotokozerani ana zakufunika kolandira
katemera wa HPV kuti amvetsetse za katemerayu
? Mafumu limbikitsani anthu anu kukalandiritsa atsikana
katemera wa HPV kuti atetezedwe ku k h a n s a y a
chiberekero
? Msungwana, dziteteze ku khansa yakhomo la
chiberekero. Landira katemera wa HPV.
? Amayi a msinkhu wobereka kayezetseni khansa
yakhomo la chibelekero kuti ngati muli nayo
muthandizidwe zisanafike povuta
? Makolo fotokozerani ana zakufunika kolandira
katemera wa HPV kuti amvetsetse za katemerayu.
Mukafuna kudziwa zambiri, kafunseni kwa adokotala
kuchipatala chapafupi ndi inu
Produced by Health Education Unit in collaboration with EPI,
RHU, NCD with support from WHO, CHAI, GAVI (2013)
Mau oyamba Nanga HPV imafala bwanji?
Unduna wa za Umoyo wakhala ukuona anthu ochuluka HPV imafala kuzera mu kugonana
odwala matenda a Khansa omwe akumafika kuzipatala
Kodi angatenge HPV ndani?
zosiyanasiyana. Khansa ndi matenda omwe akhoza
Aliyense yemwe anayamba mchitidwe ogonana angathe
kugwira chiwalo chilichonse ndipo wodwala akapanda
kutenga HPV. Ngakhale kuti wina aliyense angatenge HPV,
kupeza chithandizo choyenera msanga, matendawa
ndi akazi okha omwe angadwale khansa ya khomo
amafalikira ziwalo zina.
lachiberekero. Munthu yemwe ali ndi HPV samva
Mwamitundu ya Khansa yonse, khansa yakhomo la kupweteka pena paliponse
chiberekero ndi yomwe ili yochuluka kwambiri mwa
Kodi zomwe zingapangitse kuti munthuatenge
amayi. Chaka chilichonse amayi opitirira 2,300 amadwala
HPV ndi ziti?
matendawa ndipo opitirira 1,600 amamwalira.
? kugonana ndi amuna kapena akazi ambiri
Chifukwa cha kukula kwa vutoli, boma lakonza ? Kuyamba mchitidwe ogonana ukadali mwana
ndondomeko yopereka katemera wa Human Papilloma ? Kugonana ndi mwamuna kapena mkazi yemwe
Virus (HPV) kwa atsikana ndi cholinga chowateteza amagonana ndi anthu ambiri.
kumatenda a khansa ya khomo la chiberekero. HPV ndi ? Kukhala ndi matenda ena opatsirana pogonana.
kachirombo komwe kamayambitsa matendawa. ? Kutsika kwa chitetezo mthupi pa zifukwa zina m o n g a
Katemerayu ayamba kuperekedwa mu maboma a Rumphi HIV ndi Edzi
ndi Zomba mu September, 2013.
Kodi tingapewe bwanji Khansa ya khomo la
Kodi khansa ya khomo la chiberekero ndi chiyani? chiberekero?
Iyi ndi khansa yomwe imagwira khomo la chibelerekero. ? Kulandiritsa atsikana katemera wa HPV
Ngati amayi salandira chithandizo msanga, khomo la ? Kuyamba kuyezetsa khansa ya khomo la
chiberekero limawonongeka ndipo kuwonongekako chiberekero amayi akakwanitsa zaka 15
kungathe kumafalikira ziwalo zina. ? Kupewa kugonana ndi anthu ambiri
? Kugwiritsa ntchito makondomu
Ziizindikiro za khansa ya khomo lachibelekero ndi
? Kupewa mchitidwe ogonana ukadali mwana
ziti?
? Kuchita mdulidwe wa abambo
? Munthu amene ali ndi khansa ya khomo
lachibelekero saonetsa zizindikiro msanga Kodi katemera wa HPV amagwira ntchito bwanji?
mpakana matenda atakula. Katemerayu amateteza atsikana ku kachirombo ka HPV
? Mayi amataya magazi akangotha kugonana. komwe kamayambitsa khansa ya khomo la chiberekero
? Kutaya magazi kwa mzimayi amene anasiya mtsogolo.
kusamba.
? Mayi kutaya magazi nthawi imene sakuyenera Kodi oyenera kulandira katemera wa HPV ndani?
kusamba Katemerayu
? adziperekedwa mumasukulu kwa
? Kutulutsa chikazi chochuluka chosintha mtundu, atsikana onse a sitandade 4.
komanso chafungo. ? Atsikana omwe sali pa sukulu, ngati akwanitsa zaka
? Kumva kupweteka mchiuno, mwendo ndi msana. 10 adzikalandira katemerayu ku zipatala zonse za
boma ndi za mishoni komanso malo onse o m w e
Kodi chimayambitsa khansayi ndi chiyani? kumachitikira sikelo ya ana.
Khansayi imayamba ndi kachirombo kotchedwa Human
PapillomaVirus (HPV). Kodi katemerayu amaperekedwa bwanji?
? Katemerayu ndiwobaya pa mkono.

You might also like