KUPHUNZITSA
MA ADVENTURER
2025 CMC LEADERSHIP SEMINAR
24TH -26TH JANUARY, 2025
MATHEWS ALBERTO MALUNGA
MAVESI OTSOGOLERA
• MASALIMO 25 V 4
• DETRONOMO 11 VESI 19
• DETRONOMO 6 VESI 7
CHOLINGA CHOPHUNZITSA MA
ADVENTURER
• MBALI IYI IMALIMBIKITSA UBALE PAKATI PA
NDIMAKOLO KOMANSO KULIMBIKITSA KUKULA KWA
ANA KU UZIMU, THANZI, KAGANIZIDWE KOMANSO
CHIKHALIDWE
KAPHUNZITSIDWE KABWINO
NDIKOTANI?
• KOPATSIRANA/KUPANGIRA LIMODZI
• KUPANGA NDIMWANA PAYEKHA
• KUGWIRITSA NTCHITO ZONSE ZOMWE MULUNGU
ANATIPATSA MONGA KUONA, KUMVA, KUKHUDZA
• KUMUMVERA MWANA
• KUPANGA ZINTHU ZOMWE SANGAZIIWALE
PANGANO LA MA
ADVENTURER
• CHIFUKWA YESU AMANDIKONDA, NTHAWI ZONSE
NDIDZAYESA KUCHITA UBWINO WANGA OPAMBANA
LAMULO
• OMVERA
• WANGWIRO
• OONA
• OKOMA MTIMA
• WAULEMU
• OMVETSERA BWINO
LAMULO
• OTHANDIZA
• OSANGALALA
• OGANIZA BWINO
• WAULEMU KWA MULUNGU
MAKALASI
• LITTLE LAMB
• EARLY BIRD
• BUSY BEE
• SUNBEAM
• BUILDER
• HELPING HAND
KUKONZEKERA KALASI
• DZIWANI ZOKUYENEREZANI(REQUIREMENTS)
• KHALANI PANSI NDI MAKOLO ADZIWE UDINDO WAWO
• PANGANI PULANI YAPACHAKA
• PULANI YAZOMWE MUYENERA KUPHUNZITSA
PASABATA KAPENA PATSIKU
• KONZANI NTHAWI YOYENERA KUPHUNZITA-KALASI
ISAPOSE MPHINDI MAKUMI ATATU
ZOYENERA KUPHUNZITSA
ANA
• FOUR INSTRINSIC RELATIONSHIPS IN A CHILD’S LIFE
• 1. MY GOD ( Mwana ndi Mulungu) mwana amaphunzira nkhani
zosangalatsa zokhudzana ndi mkangano waukulu komanso ubale wake
ndi Mulungu amene wapanga zazikulu kwaiye
• 2. MY SELF ( Zaiye mwana) zochitika zomwe zingamuthandize
kuyamikira luso lake komanso kukulitsa ukadaulo wake
• 3. MY FAMILY ( Mwana ndi apabanja ake) kulimbikitsa mwana kupanga
ubale wanwino ndiena
• 4. MY WORLD ( Mwana ndi Dziko) kutsogolera ana kudziwa zambiri
zadziko komanso zomwe Mulungu analenga komanso udindo wawo
poasamala chilengedwe
MY GOD
KUPHUNZITSA KUKULA KOMANSO UBALE
WAMPHAMVU PAKATI PA MWANA NDI MULUNGU
• PULANI YOMPULUMUTSIRA MWANA-GOD’S LOVE,
UCHIMO, KUKHULULUKA, KULAPA NDI KUMVERA
• UTHENGA WAKE KWA MWANA-MAVESI OLOWEZA,
KUWERENGA BIBLE
• MPHAMVU YA MULUNGU MMOYO WAMWANA-
PEMPHERO, BIBLE STUDY,MAUMBONI KOMANSO
KUKHALA MOTUMIKIRA YESU
MY SELF
• I AM SPECIAL-ADZIWE LUSO LAKE KOMANSO UDINDO
WAKE POTUMIKIRA
• NDITHA KUPANGA CHISANKHO CHOYENERA-
KAPANGIDWE KAZISANKHO, MMENE AMAMVERA
• NDITHA KUSAMALA THUPI LANGA-THANZI, MAFIZO,
MADYEDWE, UKHONDO
MY FAMILY
KUMULIMBIKITSA KUKHALA OKONDWA
KOMANSO OPAMBANITSA ZINTHU PAKATI
PABALE NDANZAKE
• KUPAMBANA KWABANJA LAKE, UDINDO WAKE
• ULEMU, KUYAMIKIRA KOMANSO KUTENGA NAWO
MBALI PA ZAPAKHOMO
• CHITETEZO CHAKE, UDINDO WACHIKHRISTU,
NDIMALUSO ENA
MY WORLD
KULIMBIKITSA MWANA KUTI AKHALE MDZIKO
NDI KUDZIDALIRA KOMANSO KUDZIPEREKA
• PEER PRESSURE, SOCIAL SKILLS
• KUTUMIKIRA PAMPINGO, KUDERA, MDZIKO
• NATURE RECREATION KUKHUDZIDWA
PACHILENGEDWE
ZOFUNIKA KUZIGANIZIRA
POKONZA PHUNZIRO
• 1. CLASS CONTENT-UDZIWE CHOLINGA
CHAPHUNZIRO NDIZOMWE APHUNZIRE
• UZIDZIWE ZOKAPHUNZITSAZO
• UPEZE MABUKU OFUNIKIRA NDIZINA ZOMWE
UNGAGWIRITSE NTCHITO
• 2 KUPEZA ZIPANGIZO NDINJIRA ZOPHUNZILIRA
• CLASS ABILITY-KUTHEKERA KWA KALASI
PAKAPHUNZIRIDWE
KUPITILIZA……..
• 4. ZOMWE MWANA AKUDZIWA KALE-ZIMATHANDIZA
KUDZIWA MODUTSA
• 5. NTHAWI-PEREKANI NTHAWI YOYENERA
POPHUNZITSA
• KUMADZIWA NYENGO-SOME TOPICS MAY BE TAUGHT
EFFECTIVELY IN ONE SEASON AND NOT IN ANOTHER
CHOFUNIKIRA KUDZIWA
NDICHANI
• TIKHALE NDI WORKBOOK YOMWE ITITHANDIZE
KAPHUNZITSIDWE KOMANSO MAYESO A ANA
( ASSESMENT)
• TITSATIRE BWINO WORKBOOK CHIFUKWA NDIYOMWE
IPANGITSE NTCHITO YATHU KUPEPUKE KWAMBIRI
• ATSOGO, TIYENI KOGWIRA
ZIWALA
• NDUFUNA MAYI ANGA
DZIOMBERENI MMANJA
• MAFUNSO????